Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Georgia

Aerodromis Dasahleba 13th Street, No. 10

TBILISI, 0182

GEORGIA

+995 32-276-23-59

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:30 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 3:30 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 30

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’Chiazebaijani, Chijojiya, Chisiriki cha Chikadishi. Timajambulanso mavidiyo ndi zinthu zina zomvetsera m’zinenero zina.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.