Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

France

2 rue Saint-Hildevert

27400 LOUVIERS

FRANCE

+33 2-32-25-55-55

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:00 a.m., 10:00 a.m., 2:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’zinenero 4. Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku France ndi madera ena amene amalankhula Chifulenchi ngati (Guadeloupe, Martinique, French Guiana, La Réunion, Mayotte, Saint Pierre ndi Miquelon).

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.