Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Finland

Puutarhatie 60

FI-01300 VANTAA

FINLAND

+358 9-825-885

Kuona Malo

Lolemba Mpaka Lachisanu

9:00 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timasindikiza magazini 30 miliyoni, timabuku ndiponso timapepala m’zinenero zoposa 100 chaka chilichonse. Timatumiza matani 127 a mabuku ndi zinthu zina chaka chilichonse ku Russia ndiponso kumayiko ozungulira nyanja ya Baltic.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.