Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Fiji

19 St. Fort Street

SUVA

FIJI

+679 330-4766

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito ya Mboni za Yehova ku Fiji, Kiribati, Tuvalu ndi Nauru. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chifiji, Chikiribati, Chituvalu, Chirotumani ndiponso Chinauru.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.