Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Ethiopia

Mboni za Yehova, Yeka sub-city, Wereda 12;

Nyumba 161, m’mbali mwa Kotebe Road; kupitirira pang’ono kilomita imodzi

Kotebe College for Teachers Education

ADDIS ABABA

ETHIOPIA

+251 11-660 3611

+251 91-121-3489 (Foni yam’manja)

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:20 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero zisanu za ku Ethiopia. Timayang’anira ntchito yophunzitsa Baibulo m’dzikoli komanso m’maiko ena oyandikana nawo. Timayang’aniranso ntchito yomanga Nyumba za Ufumu.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.