Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Central African Republic

58 rue du Stade Boganda

BANGUI

CENTRAL AFRICAN REPUBLIC

+236 21-61-20-70

+236 21-61-89-25

+236 70-11-08-00

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito ya Mboni za Yehova yophunzitsa anthu Baibulo komanso yomanga Nyumba za Ufumu ku Central African Republic ndiponso ku Chad. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chisango komanso m’zinenero zina 7.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.