Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Canada

13893 Highway 7

GEORGETOWN, ON L7G 4S4

CANADA

+1 905-873-4100

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 10:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timasindikiza magazini oposa 255 miliyoni chaka chilichonse. Timatumiza mabuku olemera matani 6,000 m’zinenero pafupifupi 300 chaka ndi chaka.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.