Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Cameroon

Les Témoins de Jéhovah du Cameroun

Ancienne Route SONEL

Bonamikano, Bonabéri,

DOUALA

CAMEROON

+237 3339-0250

+237 3339-2101

Kuona Malo

Lachitatu ndi Lachisanu

2:00 p.m. mpaka 4:30 p.m.

Nthawi yonse: Mphindi 30

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene anthu a Mboni za Yehova oposa 40,000 akugwira m’mayiko a Cameroon, Gabon ndi Equatorial Guinea. Timatumiza mabuku m’mayiko asanu a ku Africa.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.