Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Bulgaria

Boulevard Tsar Boris III 227

1618 SOFIA-PAVLOVO

BULGARIA

+359 2-9559-590

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timayang’anira mipingo ndi magulu pafupifupi 60 ku Bulgaria. Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’Chibugariya, Chinenero Chamanja cha ku Bulgaria ndiponso Chiromane.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.