Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Britain

Watch Tower

The Ridgeway

LONDON

NW7 1RN

ENGLAND

+44 20-8906-2211

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m. Pa ola lililonse anthu amayamba kuona malo.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Chaka chilichonse timasindikiza timabuku ndi magazini oposa 200 miliyoni ndipo timatumiza mabuku amenewa m’mayiko osiyanasiyana 100. Alendo odzaona malo amaonanso zithunzi zambiri yakale zochedwa: “Mbiri ya Baibulo ku Britain.”

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.