Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Belgium

Christian Congregation of Jehovah’s Witnesses

rue d’Argile-Potaardestraat 60

B-1950 KRAAINEM

BELGIUM

+32 2-782-00-15

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:30 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timayang’anira ntchito imene Mboni za Yehova zikugwira ku Belgium. Alendo odzaona malo amaonanso zinthu za mbiri yakale zokhudza Mboni za Yehova.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.