Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Australia

12-14 Zouch Road

DENHAM COURT NSW 2565

AUSTRALIA

+61 -9829-5600

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

10:00 a.m. mpaka 12:00 p.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 3:00 p.m.

Nthawi yonse: Maola awiri

Zimene Timachita

Timasindikiza ndi kutumiza magazini oposa 18 miliyoni m’zinenero zoposa 55 kumayiko ndi zilumba zapanyanja ya Pacific.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.