Pitani ku nkhani yake

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Armenia

38 Keri Street

0028 YEREVAN

ARMENIA

+374 10 708 200

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

9:30 a.m. mpaka 11:⁠00 a.m. komanso 2:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Muyenera kuimba foni kuti munene tsiku komanso nthawi imene mukufuna kudzaona malo.

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza Baibulo m’Chiameniya, zilembo za a akhungu za Chiameniya, Chinenero Chamanja cha ku Armenia ndi Chirabakhi. Timayang’anira ntchito ya a Mboni za Yehova okwana ??? m’dziko la Armenia. Alendo odzaona malo amaonanso zinthu za mbiri yakale zokhudza Mboni za Yehova.