Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

Mfundo Zokhudza Maofesi Ndiponso Kuona Malo

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu komanso malo athu osindikizira mabuku ndipo tidzakulandirani ndi manja awiri. Dziwani malo amene kuli maofesiwa komanso nthawi imene mungaone malo.

 

Argentina

Roseti 1084

C1427BVV CDAD. AUT. DE BUENOS AIRES

ARGENTINA

+54 11-3220-5900

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 2:00 p.m. mpaka 4:30 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku a nkhani za m’Baibulo m’Chinenero Chamanja cha ku Argentina ndiponso m’zinenero zina zinayi. Timasindikiza magazini, timabuku, timapepala ndi zinthu zina zomwe timatumiza m’mayiko a Argentina, Uruguay ndi Chile.

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.