Kuona Malo ku Beteli

Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.

Kazakhstan

Christian Center of Jehovah’s Witnesses

187 Auezov Street,

Kalkaman-2 micro-district,

ALMATY, 050006

KAZAKHSTAN

+7 727 232-36-62

+7 727 226-30-42

+7 777-223-19-89 (Foni Yam’manja)

Kuona Malo

Lolemba mpaka Lachisanu

8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.

Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timachita

Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chikazakhi (Chisililiki), Chikazakhi (cha ku Arabia) ndiponso Chiwiga (Sililiki).

Koperani pepala losonyeza ofesi yathu.