Pitani ku nkhani yake

Tizikumbukira Imfa ya Yesu

Tizikumbukira Imfa ya Yesu

Chaka chilichonse a Mboni za Yehova amakumbukira imfa ya Yesu mogwirizana ndi zimene iye ananena. (Luka 22:19, 20) Tikukuitanani kuti mudzakhalepo pamwambo wofunika kwambiri umenewu. Mudzaphunzira mmene moyo ndiponso imfa ya Yesu zingakuthandizireni.