ONANI

Pangani Dawunilodi:

 1. 1.1. Timasankha zochita nthawi zonse

  Pa zosangalatsa ndi zauzimu.

  Pali nthawi yoseka ndi anzathu,

  Koma tisangokhalira zimenezo.

  (KOLASI)

  Tizipeza nthawi ya zinthu zofunika—

  Pemphero, kuphunziranso,

  N’kudzipereka: Izi n’zofunikadi.

  Titayedi zolemetsa

  Nthawi yatsalayi yafupika

  Tiyesetse kuchita zofunikazi

 2. 2. Chikhulupiriro chingachepe

  Vuto la zachuma likatikhudza.

  Koma tipezeke pakhomo.

  Tithandize banja lathu kukonda M’lungu​—⁠

  (KOLASI)

  Tizipeza nthawi ya zinthu zofunika—

  Pemphero, kuphunziranso,

  N’kudzipereka: Izi n’zofunikadi.

  Titayedi zolemetsa

  Nthawi yatsalayi yafupika

  Tiyesetse kuchita zofunikazi

  (KOLASI)

  Tizipeza nthawi ya zinthu zofunika—

  Pemphero, kuphunziranso,

  N’kudzipereka: Izi n’zofunikadi.

  Titayedi zolemetsa

  Nthawi yatsalayi yafupika

  Tiyesetse kuchita zofunikazi