ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

Pangani Dawunilodi:

 1. 1. Waona akukula,

  M’zaka zonse

  Mtendere m’mavuto,

  Zamuphunzitsa.

  Nthawi zonse akasankha mwanzeru,

  Atate amakondwa.

  (KOLASI)

  Mwana wake wapaderayu.

  Sangasiye kumukonda.

 2. 2. Amadzipereka—

  Nthawi zonse.

  Malangizo ake

  Amuthandiza,

  Amasangalala

  Amam’kondadi.

  Amamva bwino akamva:

  (KOLASI)

  “Mwana wanga wapaderawe.

  Sin’ngasiye kukukonda.”

  (VESI LOKOMETSERA)

  Inde Yehova

  Amaonadi

  Zabwino zonse

  Ndi chikondi chako.

  Sangayiwale

  Umakondadi

  Dzina lake.

  (KOLASI)

  Mwana wake, eeh, wamkaziyu.

  Mwana wake, adzam’thandiza.

  Mwana wake, adzam’samala.

  Mwana wake, amam’konda.