Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano

 Nyimbo 154

Tipirirabe Mpaka Mapeto

Tipirirabe Mpaka Mapeto

(Mateyu 24:13)

 1. Tiyenera

  kumapirira mayesero.

  Paja Yesu

  anachitanso zimenezo.

  Analimba mtima,

  podalira Mlungu.

  (KOLASI)

  Tikhale opirira

  tizilalikira.

  M’lungu amatikonda.

  Adzatithandiza kupirira.

 2. Tingakumane

  ndi mavuto ochuluka,

  komabe moyo

  wosatha tidikirira.

  Mtendere wosatha

  tiulakalaka.

  (KOLASI)

  Tikhale opirira

  tizilalikira.

  M’lungu amatikonda.

  Adzatithandiza kupirira.

 3. Sitichita

  mantha kapena kukayika.

  Titumikire

  mpaka tsiku lomaliza.

  Tsiku la Yehova

  lilidi pafupi.

  (KOLASI)

  Tikhale opirira

  tizilalikira.

  M’lungu amatikonda.

  Adzatithandiza kupirira.