Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova—Nyimbo Zatsopano

 Nyimbo 147

Chuma Chapadera

Chuma Chapadera

(1 Petulo 2:9)

 1. Odzozedwa ndi mtundu,

  Watsopano wa M’lungu.

  Iye anawagula,

  Padziko lapansi.

  (KOLASI)

  N’chuma chapadera,

  Otchedwa dzina lanu

  Amakukondani.

  Amalengezadi za inu.

 2. Ndi mtundu woyeradi,

  Wophunzitsa cho’nadi.

  Mulungu wawapatsa

  Kuwala kwakedi.

  (KOLASI)

  N’chuma chapadera,

  Otchedwa dzina lanu

  Amakukondani.

  Amalengezadi za inu.

 3. Amasonkhanitsanso,

  Nkhosa zina mwakhama.

  Ndi okhulupirika.

  Kwa Mwanawankhosa.

  (KOLASI)

  N’chuma chapadera,

  Otchedwa dzina lanu

  Amakukondani.

  Amalengezadi za inu.