Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 98

Malemba Anauziridwa ndi Mulungu

Sankhani Zoti Mumvetsere
Malemba Anauziridwa ndi Mulungu
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(2 Timoteyo 3:16, 17)

 1. 1. M’dzikoli, Mawu a M’lungu,

  Amatiunikira.

  Tikawagwiritsa ntchito,

  Tidzakhala omasuka.

 2. 2. Mawu ndi ouziridwa,

  Amatiphunzitsadi.

  Amawongoladi zinthu,

  Ndiponso kutilangiza.

 3. 3. Mawu a Mulungu wathu,

  Amatiphunzitsatu.

  Ngati timawawerenga

  Azititsogoleradi.