Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 93

Mudalitse Msonkhano Wathu

Sankhani Zoti Mumvetsere
Mudalitse Msonkhano Wathu
ONANI

(Aheberi 10:24, 25)

 1. 1. Pamsonkhanowu Yehova,

  Tipempha m’tidalitse.

  Ndifetu oyamikira;

  Mzimu ukhale nafe.

 2. 2. M’tithandize kumvetsetsa;

  Mfundo za choonadi.

  M’tiphunzitse kulalika;

  Tikhale achikondi.

 3. 3. Mudalitse misonkhano;

  Mutipatse mtendere.

  Mawu ndi zochita zathu

  Zikulemekezeni.