Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 80

“Tawalani Ndipo Muona Kuti Yehova Ndi Wabwino”

Sankhani Zoti Mumvetsere
“Tawalani Ndipo Muona Kuti Yehova Ndi Wabwino”
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Salimo 34:8)

 1. 1. Kutumikira Mulungu;

  Kumatisangalatsadi.

  Ntchito n’njambiri yolalikira,

  Timaipezera nthawi.

  (KOLASI)

  M’lungu akuti: ‘Talawani​​—

  Inetu ndi wabwino.’

  Timapindula tikachita,

  Zonse zomwe tingathe.

 2. 2. Mtumiki wanthawi zonse,

  M’lungu amamudalitsa.

  Amamupatsa zofunikira,

  Amakhala wokhutira.

  (KOLASI)

  M’lungu akuti: ‘Talawani​​—

  Inetu ndi wabwino.’

  Timapindula tikachita,

  Zonse zomwe tingathe.