Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 79

Athandizeni Kukhala Olimba

Sankhani Zoti Mumvetsere
Athandizeni Kukhala Olimba
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Mateyu 28:19, 20)

 1. 1. Kuphunzitsa nkhosa za M’lungu

  Ndi mwayi wapadera.

  Yehova wawatsogolera

  Amakonda cho’nadi.

  (KOLASI)

  Yehova tikupemphatu

  Kuti muziwateteza.

  Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe

  Akhale olimba.

 2. 2. Mayesero akawagwera,

  Tinkawapempherera.

  Tinawaphunzitsa mwakhama;

  Pano adalitsidwa.

  (KOLASI)

  Yehova tikupemphatu

  Kuti muziwateteza.

  Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe

  Akhale olimba.

 3. 3. Akhale okudalirani,

  Inu M’lungu ndi Yesu.

  Apirire pamayesero,

  Akalandire moyo.

  (KOLASI)

  Yehova tikupemphatu

  Kuti muziwateteza.

  Mwa Yesu tikupemphani: Athandizenibe

  Akhale olimba.