Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 72

Tikulalikira Choonadi Chonena za Ufumu

Sankhani Zoti Mumvetsere
Tikulalikira Choonadi Chonena za Ufumu
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Machitidwe 20:20, 21)

 1. 1. Poyamba sitinkadziwa

  Zinthu zoti tizichita.

  Yehova ’natumiza

  Choonadi ndi kuwala.

  Ndipo tinazindikira

  Chifuniro cha Yehova,

  Kuti tim’tumikire

  Ndi kumalengeza dzina lake.

  Timalalikira ndithu

  Pamakomo ndi mumsewu.

  Timathandiza anzathu

  Choonadi achidziwe.

  Tiyeni tiziyesetsa

  Kutumikira Mulungu,

  Kufikira Yehova

  Atanena kuti tamaliza.