Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 64

Tizigwira Ntchito Yokolola Mosangalala

Sankhani Zoti Mumvetsere
Tizigwira Ntchito Yokolola Mosangalala
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Mateyu 13:1-23)

 1. 1. Tili munthawi yokolola,

  Ndi mwayidi waukulu.

  M’mindamo tirigu wachanso,

  Tiyenitu tikolole.

  Yesu akutitsogolera,

  Ndi chitsanzo chabwinotu.

  Timakhala osangalaladi.

  Kugwira nawo ntchitoyi.

 2. 2. Timakonda M’lungu ndi anthu,

  Choncho timachita khama.

  Tiphunzitse anthu mwachangu,

  Mapeto ayandikira.

  Yehova amatidalitsa,

  Timakhala achimwemwe.

  Tipirire pogwira ntchitoyi,

  M’lungu adzatithandiza.