ONANI

(Mateyu 22:37)

 1. 1. Tengani mtima wanga

  Cho’nadi uzikonda.

  Tengani mawu anga

  Ndikuimbirenitu.

 2. 2. Tengani mapaziwa;

  Akutumikireni.

  Chuma changa tengani.

  Sindingakumaneni.

 3. 3. Tengani moyo wanga,

  Chifuniro chanucho,

  Ndizichichita ndithu

  Ndikusangalatseni.