ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Salimo 54)

 1. 1. Atate mumve nyimbo yanga.

  M’lungu wanga ine ndi wanu.

  Dzina lanu ndi lalikulu.

  (KOLASI)

  Yehova mumve pempheroli.

 2. 2. Ndathokoza ndadzuka bwino,

  Mwandipatsa mphatso ya moyo.

  Mumandisangalatsa mtima.

  (KOLASI)

  Yehova mumve pempheroli.

 3. 3. Ndifuna kuchita zabwino.

  Ndiyendetu m’kuwala kwanu.

  Ndipirire mavuto onse.

  (KOLASI)

  Yehova mumve pempheroli.