ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Chivumbulutso 11:15; 12:10)

 1. 1. Yehova Mulungu wathu,

  Ndinu wamuyaya.

  Mwapatsa Yesu Ufumu,

  Mwa kufuna kwanu.

  Ufumu udzalamula

  Padziko lonse lapansi.

  (KOLASI)

  Zafika tsopano

  Ufumu chipulumutso.

  Ufumu wayamba.

  Tipempha kuti: “Ubwere!”

 2. 2. Nthawi ya Satana yatha;

  Dziko latsopano

  Lili pafupi kwambiri.

  Mavuto adzatha.

  Ufumu udzalamula

  Padziko lonse lapansi.

  (KOLASI)

  Zafika tsopano

  Ufumu chipulumutso.

  Ufumu wayamba.

  Tipempha kuti: “Ubwere!”

 3.  3. Angelo asangalala,

  Aimba mokondwa.

  Satana wachotsedwako,

  Onse akondwera.

  Ufumu udzalamula;

  Padziko lonse lapansi.

  (KOLASI)

  Zafika tsopano

  Ufumu chipulumutso.

  Ufumu wayamba.

  Tipempha kuti: “Ubwere!”