Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 21

Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba

Sankhani Zoti Mumvetsere
Pitirizani Kufunafuna Ufumu Choyamba
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(Mateyu 6:33)

 1. 1. Chofunika kwa Yehova,

  Chomwe chim’sangalatsa,

  Ndicho Ufumu wa Khristu,

  Womwe ukonze zonse.

  (KOLASI)

  M’fune Ufumu choyamba

  Ndi chilungamo chake.

  M’tamandeni mumitundu,

  Ndi kum’tumikirabe.

 2. 2. Musade nkhawa n’zamawa,

  Za chakudya ndi madzi

  M’lungu adzatipatsatu

  Tikafuna Ufumu.

  (KOLASI)

  M’fune Ufumu choyamba

  Ndi chilungamo chake.

  M’tamandeni mumitundu,

  Ndi kum’tumikirabe.

 3. 3. Choncho muzilalikira;

  Muzithandiza ena

  Kudaliranso Yehova

  Ndi Ufumu wakenso.

  (KOLASI)

  M’fune Ufumu choyamba

  Ndi chilungamo chake.

  M’tamandeni mumitundu,

  Ndi kum’tumikirabe.