Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

 NYIMBO 140

Tidzapeza Moyo Wosatha

Sankhani Zoti Mumvetsere
Tidzapeza Moyo Wosatha
ONANI

(Yohane 3:16)

 1. 1. Onani m’maganizo,

  Anthuwo pamtendere.

  Chisoninso chathadi!

  Kulira kwathanso.

  (KOLASI)

  Imbani mokondwa!

  Ngakhale inunso.

  Patsikulo mudzati,

  “Moyo wosathadi!”

 2. 2. Anthu sadzakalamba.

  M’lungu adzawakonda.

  Mavutowa adzatha,

  Anthu sadzalira.

  (KOLASI)

  Imbani mokondwa!

  Ngakhale inunso.

  Patsikulo mudzati,

  “Moyo wosathadi!”

 3. 3. Tidzasangalalatu

  Poimbira Mulungu.

  Tizidzalemekeza

  Yehova Mulungu.

  (KOLASI)

  Imbani mokondwa!

  Ngakhale inunso.

  Patsikulo mudzati,

  “Moyo wosathadi!”