Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

MITU YA NKHANI

Mboni za Yehova

Chichewa

Imbirani Yehova Mosangalala

 NYIMBO 123

Tizigonjera Mulungu Mokhulupirika

Sankhani Zoti Mumvetsere
Tizigonjera Mulungu Mokhulupirika
ONANI
Kukula kwa Zilembo
Chithunzi

(1 Akorinto 14:33)

 1. 1. Tikamalengeza padziko lonse

  Cho’nadi cha Ufumu wa Mulungu,

  Tizitsatira malangizo ake

  Tizichita zonse mogwirizana.

  (KOLASI)

  Tizigonjera Mulungu wathu,

  Mokhulupirika.

  Amatikonda, amateteza,

  Tikhulupirikedi.

 2. 2. M’lungu watipatsa mzimu woyera,

  Ndi kapolo azititsogolera.

  Choncho tizisangalatsa Yehova,

  Polalikira mokhulupirika.

  (KOLASI)

  Tizigonjera Mulungu wathu,

  Mokhulupirika.

  Amatikonda, amateteza,

  Tikhulupirikedi.