A Monica Richardson anaphunzira kuti zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina ndipo ankazikhulupirira kwambiri. Koma anasintha maganizo chifukwa cha zomwe ankakumana nazo pa ntchito yawo yaudokotala.