Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku mitu ya nkhani

Mboni za Yehova

Chichewa

Zimene Ena Amanena Zokhudza Mmene Moyo Unayambira

Massimo Tistarelli: Katswiri Wopanga Maloboti Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

Massimo Tistarelli: Katswiri Wopanga Maloboti Akufotokoza za Chikhulupiriro Chake

A Massimo Tistarelli ndi katswiri wopanga maloboti komanso makompyuta omwe amagwira ntchito potengera mmene maso a munthu amagwirira ntchito. Zomwe ankapeza pa ntchito yawo monga wasayansi zinawachititsa kuti ayambe kukayikira ngati zamoyo zinachitadi kusintha kuchokera ku zinthu zina.