Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Nkhani ya Yosiya Imatiphunzitsa Kukonda Yehova Komanso Kudana ndi Zoipa—Mbali Yoyamba

Nkhani ya Yosiya Imatiphunzitsa Kukonda Yehova Komanso Kudana ndi Zoipa—Mbali Yoyamba

Yosiya akukulira m’dziko loti anthu ake anasiya kutumikira Yehova ndipo ambiri amalambira Baala. Kodi Yosiya akwanitsa kukhala wokhulupirika n’kumachita zabwino pakati pa anthu oterewa?