Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

“Inu Yehova, ... Chikhulupiriro Changa Chili Mwa Inu”

Onerani vidiyoyi kuti muone mmene Hezekiya anasankhira zochita atakumana ndi mavuto ambiri. Iye anasonyeza kuti anali ndi chikhulupiriro cholimba komanso anali wokhulupirika. Hezekiya anali chitsanzo chabwino kwa Aisiraeli onse komanso ndi chitsanzo chabwino kwa anthu amene akutumikira Yehova masiku ano.