Muvidiyoyi muli mfundo za m’buku la Nyimbo ya Solomo ndipo ikufotokoza za chikondi chenicheni komanso kukhulupirika.