Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’buku la Zefaniya. M’bukuli muli ulosi wochenjeza anthu osamvera komanso amene amangochita zofuna zawo zokha.