Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’buku la Obadiya. Bukuli lili ndi uthenga wopereka chiyembekezo komanso limasonyeza kuti Yehova ndiye woyenera kulamulira.