Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zina zokhudza buku la Nehemiya. Bukuli limafotokoza za kumanganso Yerusalemu Ayuda atachoka ku ukapolo wa ku Babulo.