Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule zokhudza buku la Nahumu. Bukuli limafotokoza ulosi umene umasonyeza kuti Yehova amachita zonse zimene wanena komanso kuti amadana ndi chiwawa.