Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo za m’buku la Mlaliki. Bukuli lili ndi mfundo zomwe zingatithandize kukhala ndi moyo wosangalala.