Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zili m’buku la Masalimo. Bukuli lili ndi uthenga umene ungakulimbikitseni panopa komanso kukuthandizani kudziwa zinthu zabwino zimene Mulungu achite m’tsogolo muno.