Onerani vidiyoyi yomwe ikufotokoza mwachidule mfundo za m’buku lomaliza m’Malemba Achiheberi. M’bukuli muli ulosi womwe umasonyeza kuti Yehova sasintha mfundo zimene amayendera, ndi wachifundo komanso wachikondi.