Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule zokhudza ulosi womwe uli m’buku la Habakuku. Kuwerenga mfundo zimenezi kungatilimbikitse pa nthawi ya mavuto.