Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zina zokhudza buku la Ezara. Bukuli limafotokoza zimene zinachitika pobwezeretsa kulambira koona ku Yerusalemu Ayuda atachoka ku ukapolo ku Babulo.