Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zina zokhudza buku la Esitere. Bukuli limasonyeza zimene Esitere anachita molimba mtima pothandiza anthu a Mulungu.