Onerani vidiyoyi yomwe ili ndi mfundo zachidule za m’buku la Danieli. M’bukuli muli ulosi wonena za kugwa kwa maufumu amphamvu padziko lonse kuyambira ndi Babulo mpaka kuyamba kwa ulamuliro wa Ufumu wa Mulungu.