Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Agalatiya

Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Agalatiya

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe mfundo zachidule za m’kalata yopita kwa Agalatiya. Kalatayi ikusonyeza chifukwa chake tinganene kuti mbewu ya Abulahamu ikuimira Khristu ndi odzozedwa omwe adzalamulire naye limodzi.