Achinyamata ambiri amaona kuti kupeza anzawo ocheza nawo n’kovuta. Onani zimene Tara anachita kuti apeze anzake abwino omwenso amamukonda. Kenako muganizire zimene inunso mungachite kuti mupeze anzanu abwino. Muonanso zimene achinyamata a m’mayiko osiyanasiyana anachita kuti apeze anzawo abwino.